MULUNGU ANALANGA KUSAMVERA KWA ADAMU MOTANI?

from Mafunso ndi Mayankho Vol. 2: KUGWA NDI CHIPULUMUTSO (Chichewa) by Dana Dirksen

/

lyrics

4. MULUNGU ANALANGA KUSAMVERA KWA ADAMU MOTANI?

Minga, zilonda ndi minga, zilonda ndi minga
Zilonda yotembereredwa nthaka
Minga, zilonda ndi minga, zilonda ndi minga,
Zilonda masiku a moyo wonse
 
Zowawa, zokhoma, zowawa, zokhoma
Zowawa zokhoma udzadya m’menemo
Zowawa zokhoma zowawa zokhoma
Zowawa masiku a moyo onse

Kuchotsedwa m’munda wa Edeni
Kugwira ntchito mnthaka yomwe anachokera
Kupirikitsidwa m’munda wa Edeni
Olondedwa ndi lupanga la moto
Mulungu analanga kusamvera kwa Adamu motani?
Chilango cha Adamu chinali
Imfa ndi kulekana ndi Mulungu
(Genesisi 3 ndime 17 mpaka 24)

credits

license

all rights reserved

tags

about

Songs for Saplings Portland, Oregon

We create lively, fun songs that attempt to deliver the deepest Biblical truths in a format that children will love.

Songs for Saplings is James and Dana Dirksen. We live in Portland, OR, and have 6 beautiful children. We thank God that He has allowed us to share the Good News that Jesus came to seek and save that which was lost.

You can learn more about us at songsforsaplings.com
... more

contact / help

Contact Songs for Saplings

Streaming and
Download help

Redeem code

Report this track or account