Kodi tiphuzira kuti kukonda ndi kumvera Mulungu?

from Mafunso Ndi Mayankho Vol. 4: Mau A Mulungu (Chichewa) by Dana Dirksen

/

lyrics

11. Kodi tiphuzira kuti kukonda ndi kumvera Mulungu?

Tiphunzira kuti kukonda?
Tiphunzira kuti kumvera Mulungu?
Tiphunzira kuti kukonda n’kumvera Mulungu?

Mu Baibulo tiphunzira kukonda
Mu Baibulo tiphunzira kumvera Mulungu
Mu Baibulo tiphunzira kukonda n’kumvera Mulungu

Sunga buku lachilamulo pakamwa pako
Liwerenge tsiku ndi tsiku
Kuti usamale mkuchita zonse zolembedwamo
Yoswa chaputala 1 vesi 8

credits

license

all rights reserved

tags

about

Songs for Saplings Portland, Oregon

We create lively, fun songs that attempt to deliver the deepest Biblical truths in a format that children will love.

Songs for Saplings is James and Dana Dirksen. We live in Portland, OR, and have 6 beautiful children. We thank God that He has allowed us to share the Good News that Jesus came to seek and save that which was lost.

You can learn more about us at songsforsaplings.com
... more

contact / help

Contact Songs for Saplings

Streaming and
Download help

Redeem code

Report this track or account