Kodi ndi ntchito zanji Khristu anachita monga Mesiya olonjezedwa?

from Mafunso Ndi Mayankho Vol. 3: Khristu Ndi Ntchito Zake (Chichewa) by Dana Dirksen

/

lyrics

8. Kodi ndi ntchito zanji Khristu anachita monga Mesiya olonjezedwa?

Ntchito zanji Khristu anachita
Monga Mesiya olonjezedwa
Mneneri, Mbusa, mfumu

Kwa ife, mwana wabadwa
Mwana wa mamuna wapatsidwa
Ndi ulamuliro uli pa phewa lache
Adzatchedwa waumphungu odabwitsa
Mulungu wamkulu , Tate wosatha
Kalonga wa mtendere
Tutu tulututu (*2)

Ntichito zanji Khristu anachita
Monga Mesiya olonjezedwa
Mneneri, M’busa, Mfumu

Yesaya vesi 6 chaputa 9
Kwaife mwana wapatsidwa
Ndi ulamuliro uli pa phewa lache
Adzatchedwa waumphungu odabwitsa
Mulungu wamkulu Tate osatha
Kalonga wa mtendere

credits

license

all rights reserved

tags

about

Songs for Saplings Portland, Oregon

We create lively, fun songs that attempt to deliver the deepest Biblical truths in a format that children will love.

Songs for Saplings is James and Dana Dirksen. We live in Portland, OR, and have 6 beautiful children. We thank God that He has allowed us to share the Good News that Jesus came to seek and save that which was lost.

You can learn more about us at songsforsaplings.com
... more

contact / help

Contact Songs for Saplings

Streaming and
Download help

Redeem code

Report this track or account